Mchinji Boma Plot yogulitsa Masautso Village around fair view secondary School pali nyumba yongoyamba umanga yolekeza mu mawindo. kukula kwa malo ndi 58 by 35 by 20 meters. Malo amapepala(title deeds). Malo ambali mwa nseu wabwino, 150m kuchoka nseu wa tarmac Magetsi ali pafupi zedi and madzi kunangotsala kulumikiza. Mtengo wokambilana, Malo apite 9.5 million kwacha. Serious buyers Contact: +265993293654/0888043786
$9,500,000