ZATENGENI MA FRIDGE AWA OCHOKERA KU SOUTH AFRICA PA MTENGO WABWINO KIC deep freezer (210 litres) sadakonzedwepo sadaonjezeredwepo gas amaumitsa mwakanthawi kochepa alibe zimbiri mkati paint ndi original sadatsithidwepo chilichonse
$350