Lero timakamalizitsa kupanga install hand press pump ku Lumbadzi.

Nthawi ndi yomwe ino, nanunso kumbitsani chanu chitsime lero. Sitingamadalire madzi a water board nthawi zonse. Mitengo yathu: kukumba Chitsime chokha, kumangira brick lining komanso Apron @ 350,000. Kukumba Chitsime ndikuika hand press pump @ 600,000. Kukumba Chitsime ndikuika Afridev pump ( Mjigo) @ 950,000. Zitsime zathu timakumba mwaukadaulo See more

FREE

seller's name'
Name: Samson K
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 31 July, 2023

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 5
product image 1
Image 2 of 5
product image 2
Image 3 of 5
product image 3
Image 4 of 5
product image 4
Image 5 of 5
Loading recommendations...