SWAP DEAL NDILI NDI SAMSUNG S7 ACTIVE 32GB NDI 4GB

Ma guyz a mu Lilongwe,amene mili ndi Tab ya Samsung yamavuto omvetsetseka tipange swap ndi ohone yangayi Samsung S7 Active,wa 3Gb ndi 4Gb ram,battry labho komanso macamera abho,4G fast Internet,vuti zima lines zo basi komanso ma cracsk wez,koma working massive 100%%%% battrry ku user mpaka 1%%%,or swap ndi phone ina,or 45 pin cash,ine ndili ku Kawale/Chilinde 1.

$45

seller's name'
Name: Chestah M
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 09 August, 2023

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 2
product image 1
Image 2 of 2