LOOKING FOR 1 ZUKU DECODER 1 GAS SOLAR BATTERY

Amene ali ndi Zuku Decoder wamkulu uja (woyambirira komanso wokhala ndi free to air channels) tiyankhulane chifukwa akufunika kwambiri. Komanso amene ali ndi ma gas battery okutha koma akuluakuku tikambirane mtengo.

FREE

seller's name'
Name: Msekanawana C
seller phone number
Location: Mzimba
uploaded on
Date: 11 August, 2023

Contact Seller