Kugulitsa nyumba ziwiri zili ku mpanda umodzi zonse. Yaikulu nd ya, three bedrooms, dinning room, sitting room, kitchen room, bathroom, yonse tilos, komanso ili nd ceiling. Ilinso nd kitchen yakunja, stores yakunja, komanso quaters ya bedroom nd sitting room. Wa rent amapereka k60,000 pa mwezi, . Inayo nd yaikulunso koma inadulidwa pakati, mbali See more
MK35