Ma Guys a mu Lilongwe,tiyeni tisinthane,ndili ndi Samsung S7 Active uyu wa 32gb ndi 4gb Ram,mavuto ndi ma lines mukuwawonawo ndi ma cracks wez. Working mbambande Ili ndi 32gb ndi 4gb ram 4G Fast Internet Fingerprint works on Home button 4000Mah Good Battery Good Cameras Both Front amd Rear Supports Wireless charging Good Sound. Mundipatsa phone yanji kupatula Mi,Chinea Moble,Itel Ndili mu Kawale/ Chilinde
$45