LETS SWAP NDILI NDI SAMSUNG GALAXY S7 ACTIVE WITH 32GB

SWAP DEAL!!!!!!! Pali S7 Active apa wa 32gb ndi 4gb Ram,ali ndi zima lines pa LCD komanso ma little cracks,monga mukuwoneramo koma koma kugwira ntchito ngati ya New One,Battrey lolimba 4000Mah,ma camera abho,4G Fast intenert,Android 8.0.0,sound ya bho,wireless charging ilimonso,very fast ku worker,ndipatseni Samsung Tab,Lenovo kapena swap ndi phone ina ngatinso Samsung,Huawei,Tecno koma ama display abwino kapena ndipatseni 45 pin Cash,kapena Laptop yofoka battry lero tikamalidzitse,Ndili mu Chilinde/ Kawale

$45

seller's name'
Name: Chestah M
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 13 September, 2023

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 3
product image 1
Image 2 of 3
product image 2
Image 3 of 3