SAMSUNG S7 ACTIVE UYU WA 32GB NDI 4GB RAM,VUTO NDI ZIMA LINES ZO NDI LITTLE CRACKS PA LCD BASI. Koma kugwira ntchito ndiye 100%,ali ndi battery labwino 4000Mah,Android 8.0.0,ma camera abwino,sound yabwino,Fingerprint pa home button komanso it supports wireless charging,ndikufuna phone ina kuoatula,Mi,Itel,Handy,Sharp ndi China Phones,Cash ndikufunapo 40 pin last yeniyeni,Chilinde/ Kawale
$45