for sale washing machine komanso amaumitsa, extra large capacity, heavy duty amene ali serious tikambilane pa 0991002635 chidziwitso: machine amenewa pakadali pano akugwira ntchito, ndipo tinagula tokha mu shop ku s.a anthu tikumasukira ma blanket ma suti ndizina zotero. Lilongwe nanjiri
$1,500