Nyumbai ili mu neighborhood ikumangwa kumene, monga mukudziwa Malo otelewa amakhala ndi manyumba amakono.. Madzi magetsi zilipo.. Ili ndi 3 bedrooms all self contain Extra toilet ndi bafa za a lendo chapa living room.. Living room Dining room Stores Kitchen.. Ayimbileni eni ake for more information: 098 308 3162
MK18