Yumba yazipinda 3 yogulisa Ku Blantyre area 12machinjiri pamtengo wa 25million kwacha. Nyumbayi ndiya safe contained,komaso master's bedroom ilindi toilet ndi bafa lake. Nyumbayi ili pafupi ndi ndi nsika komaso msewu waukulu(main road) Kuti mumve zambiri inbox me.
$25