Nyumba zogulitsa 4 malo amodzi, yayikulu yo zipinda 4,zina zamaudzuzo zipinda zitatu zitatu, floor ndi plaster zinapangidwa kale zazing'ono kunangotsala malata basi. Palinso shop yayikulu ndi ka barbershop. More
FREE