Tili NDI Isuzu iyi yayenda only 6 months in Malawi inabwera NDI Vuto la blocko Ili NDI crack Ndiye ikayenda imakweza temperature titamasula engine mpomwe timazindikilanvutoli koma it's original paint gearbox ngungungu nkhani ndiimeneyo ikufunika block Ina going at 6 million nego for more information call or wap on 0991886911/0885769599
$2