Nyumbayi ili ndi zipinda zitatu, garage, toilet ndi bathroom ndi za nkati momo. Size ndi 9 by 7 meters. Mtengo ndi 7.8 negotiable. Malo ndi lilongwe area 44.
FREE