Malo ogulitsa ku area 49 Dubai kuseli kwasent Stephano private school kufupi ndi mount meru filling station kukula kwa malo ndi 1 ecre kwa ofuna onse ndi 20 million but negotiable Kwa ofuna plot size (15 by 30) ndi 5.5 million negotiable Madzi ndi magetsi zili pafupi For viewing 0984254043 or 0886614343 PAISH GENERAL PROPERTIES
$20