Tikugulitsa ma battery amphanvu a solar antundu wa ollandia 12 v 100 ah brandnew pantengo wakale sitidakweze ngakhale pali devaluation mpaka stock yakale ithe 65,000 kwacha yomwe ija bas mutha kuonerera plasma,pa barbershop,kuunikila ma bulb,choimba,pump yothilira,ndizina zambiri tikupezeka pa banana kubangwe call 0888909491 kut mupeze lanu lero khalani osogola pogwiritsa ntchito mpanvu ya dzuwa
MK65,000