Tili ndi Malo ogulitsa ku Liwonde, malowa ali mmbali mwa nsewu wa M3 moyang'anizana ndi Ferry primary school. Kumanzere tikamachokera ku Roadblock kumanja tikamachoka ku Mangochi Turn off. Pali nyumba ziwiri Magetsi ndi madzi, palinso malo oti mutha kumanga nyumba ina ndi shop pantengo wokambirana. Mukafuna kudziwa zambiri Imbani foni kapena More
MK5