Tikugulitsa ma battery amphanvu a original antundu wa G thailand solar made in Japan mutha kuonerera plasma,kumetera pa barbershop,choimba,kutchaja ma phone,irrigating pump and many more musalolele kuthima kwamagetsi kulepheretse zintchito zanu tikupezekera ku bangwe banana stage call 0888909491 kut mupeze lanu lero ndipo simuzakhumudwa ntengo ndi 80;000 kwacha basi (brand new in cartons)
MK80,000