kodi ndinu oimba, a church, band or okondwa ndi music? khalani katakwe pophunzira luso la kaimbidwe ka zida zosiyanasiyana monga: drums, piano, guitar, violin ndi zina zambiriiii! ndi LUSO entertain ku Lilongwe . maphunzirowa akuyamba pa 8 january 2024 ndipo registration ili nkati, kuti mulembetse imbani pa 0995545449/0888114412
MK2