Plot for sale Area 44 tambalale mseu wa state house
Plot for sale Area 44 tambalale mseu wa state house, pali ma nyumba 4 omwe akukhalidwa komaso pali myumba ziwiri zosamaliza komaso pali malo akulu oti mutha kumanga zomwe mukufuna mbari mwamseu, madzi ndi magetsi zilipo zose 0995913 268.