Bulb camera

Mukufuna kuyang'anira nyumba yanu kapena business kulikose kumene muli.CCTV WIRELESS CAMERA ndi kachida kakang'ono komaso kodalirika Kamene mutha kuyang'anira katundu wanu ku user phone yanu, Mungathe kumaona video ya live, Record footage, Ndikulandira uthenga pamene motion Yapangidwa detect, Mungathe kuyankhulanaso ndi alendo Akabwera komaso ma intruders pa microphone komaso pa speaker Yapomwepo

MK38,500

seller's name'
Name: New M
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 11 December, 2023

Contact Seller