Zatolen nyumba iyi ku Lumbadzi 3bedroom and stores bathroom and toilet pali ya paja ndi nkati momwe paliso malo akulu oti pankhoza kumangidwa nyumba yaikulu ndi ma quarters. Kumvana kulipo no Agent. Contact: 0885 05 05 05
$9,500,000