PLOT FOR SALE

Plot for sale 1530, mtengo 1.5, ku area 55 kwa (Choto). Uku ndi nseu wopita ku Airport tikadzela ku area 25 Msungwi, tikadutsa Dzeza Sec Sch then tank ya water board then ndi pamene timayamba area 55. Ndi malo abwino kwambiri anthu akukukonda zedi ndipo ena akumangako monga mwawonera pa picture yoo. Misewu ilipo koma madzi ndi magetsi zizinafuke koma soon zifikako. Call or WhatsApp 0998453329 timvane

MK15

seller's name'
Name: Malawi C
seller phone number
Location: Lilongwe Area 14, Lilongwe
uploaded on
Date: 20 December, 2023

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0998453329