Malo ogulitsa ku mtiya pamanda achiwiri pamunsi pake pali nyumba ya 11 by 7.5 yomangira cement malowa ndi akulu16.5 by 12mtrs palinso uvuni kmanso popanda miyala polo la magetsi pompo madzi pompo mutha kuumbiraponso njerwa zina pompo ndalama zikufunika fast
MK4