65 acres Malo akuguritsidwa pa mtengo wa 300,000mk per acre. Malowa ali pa mtunda wa 12kms kuchoka pa Kanyenyeva, mseu wopita ku Salima. Malowa pali mtsinje ndipo ndi abwino ulimi othilira, komanso kutsegura ANIMAL RANCH. Magetsi alinso pafupi pompo. Imbani pa 0995187840.
MK300,000