MWAYIWU ukuperekedwa kwa aliyense monga oimba, ama church, ama band ndi ena tonse kuti tithe kupititsa patsogolo luso lathu olonso kuphunzira kumene mwaukadaulo ndipo kuli ma subjects monga: DRUMS, VIOLIN, GUITAR, KEYBOARD PIANO, VOCALS/VOICE NDI ZINA.
MK70