Nyumba yogulitsa ku Nancholi, pafupi ndi Nancholi CCAP, Blantyre. Nyumbayi ndi ya zipinda 4, design ya master ensuite, Koma bafa lokha lili mkati. Ku main bedroom kulinso bafa lokha. Pa sitting room Pali ma tiles komanso ku kitchen kuli sink. Mpanda unatsala mbali ziwiri osamanga koma Njerwa zake zilipo kale. Madzi alipo. Galimoto imathera kuseli kwa Neba. Kutsogolo kwa nyumba kuli space yoti patha kuima nyumba Ina. Mtengo ndi 13 million zokambirana. Call 0991003376 App 0882404905
$14