PLOT FOR SALE AT MCHEDZI VILLAGE TOWN PRICE 8. MILLION
Malo ogulitsa abwino Ali mbali mwa tala mutha kumanga chigayo olo ma shop, mages Ali pafupi kukula kwa malo 54 by 67 akupezeka ku mchedzi village town, mtengo oyambila ndi 8 million kwacha call 0996141550