Malo ogulitsa abwino Ali mbali mwa tala mutha kumanga chigayo olo ma shop mages Ali pafupi kukula kwa malo 54 by 67 akupezeka ku area 27 mchedzi pafupi ndi pa kanengo LL ndiimbileni pa 0996141550
$8