Katundu otsika mtengo uyu. Dual core 3, hdd 300gb, ram 4 gb, battery 2 hrs plus. Charger chinapoila koma chilipo, inapoilaso charging base koma ndikakhonzetsa ndekha nde mundipasa 100 pin. Delete and key ya plus inapoilaso koma ma keys ena onse ama worker bhobho, Inu amene mutha kukonzetsa nokha charging base mupeleka zingat ndilipano kunva mitengo yanu. Fast cash needed
FREE