IRON KINGS MALATA ku LILONGWE,tikupanga komaso kugulitsa malata amakono olimba komaso otsika mtengo kuposa kulikose bwelani mudzagule malata akumtima kwanu ,ubwino ogula malata kwa ife ndioti mukagula ambiri transport ndi ulere kulikose komwe inu muli, komaso ngati muli kutali mutha kungoyimba foni ndikunena mtundu wa malata omwe mukufuna ifeyo tidzabweletsa malata kwanu konko ndalama mumapeleka malata anu atafika popanda kutchajidwa ndalama ya transport.timbileni pa 0993242921
$12