Achee inuyo Kungokhara kukusangalatsani??tikhara ndi live training pa 27 January ku lilongwe LEA school (gover)komwe tikakhare tikuphunzitsa how to bake and we'll decorate a birthday cake , samoosa doghnuts rainbow freezes ND biscuits ndipo pomaliza muzagawana zomwe mwapanga thawi ya 8 o'clock mawa Kuti mupange register ndiharen pa 0985768950 or ikani ma number anu Registration 650 Fees 5 thousand
$5,000