Nyumba ndi Malo akulu ogulitsa ku Chilobwe East ntengo 4.8
Nyumba ndi Malo akulu ogulitsa ku Chilobwe East, Palinso Shop Pofika galimoto koma magesi ilibe Size ya plot 50 by 50 meters Nyumba ya 3 bedrooms Kitchen ndi storeroom Ntengo 4.8 million Contact 0991120144