Malowa size yake ndi 15 by 30 meters Madzi ndi magetsi zili pafupi Pali nyumba ziwiri zazikulu. Mtengo ndi K6 million Ngati mukufuna kudziwa zambiri ndiyimbireni pa 0992335517/0885837201
FREE