Bwerani mupeze plot pomwe pali nyumba zingapo koma zosalongotsoka muzakonza.Nyumba zili pa malo abwino pafupi ndi Sochi Manje Trading, madzi,magesi komaso nseu pofika galimoto.Ma plot alipo angapo muzasankha.Imbani 0888066796/0983980441 wap
$7