KATUNDU APITE MOYO UTSALE 4JB1 Diesel engine yosamasulako, 1 kick start, untumpered gearbox. Yolira bwino, yoyenda bwino. Muli makani umu. Machine ova sipanala. Ndipatseni MK1,850,000. Kukambirana kulipo. Call me on 0994690271. Lilongwe, area 25.
MK1,850,000