Pali Malo ogulitsa m'boma la Dedza pa roadblock side ya Mozambique. Ndi Malo a flat bwino komanso akulu bwino. TIYANKHULENI KUTI TIMVANE(only serious buy) Whapp/calls....+258865862074 iyiyi ndi mbali ya bwino Kwa amipingo komanso a business. Asakuphonyeni.
FREE