Nkhani yabwino kwaanthu okhala kuchikwawa, Nsanje komaso ndimaboma onse akumwera. Kodi mukusamuka? Muli ndi katundu ofuna kukunyamulilani? Muli ndi ulendo wafunika Galimoto?? Tafuna kukudziwitsani Kuti yankho lanu lapezeka, tili ndi Galimoto ya mtundu wa lorry ya 2 tones, imene Tingathe kukunyamulilani zinthu zanu kupititsa kulikonse Mmalawi muno pamtengo wa ziiii. Ngati mukufuna kudziwa zambili imbani phone relo pa number izi #0983555126/0999328534/0889512956.
FREE