Ife ku IRON KINGS MALATA, timapezeka ndi malata pa mtengo otsika kwambiri komaso mukatigula malata ambiri timanyamula ulere, ngati muli kutali tiuzeni type ndi color yomwe mukufuna ifeyo tidzabweletsa malata kwanu konko ndalama mumapeleka malata anu atafika tili ndi mitundu yose ya malata 0993242921
$12