Zatengeni Acer uyu very smart, battery 6 hours plus, Ram 4 GB HDD 500GB ili ndi vuto la mouse basi ndimauser external mouse koma china chilichonse chabhobho bweletsani 170pin
MK170