IRON KINGS MALATA ikukudziwitsani za kutsika mtengo kwa malata athu ndi 500 pa meter ma 26 komaso 28 gauge pomwe ma 32 gauge atsika ndi 1000 pa meter, mukagula malata ambiri transport ndi ulere kulikose komwe inu muli, ngati muli kutali koti simungathe kufika ku LILONGWE tiyimbileni foni kuti mutiuze malata omwe mukufuna ifeyo tidzabweletsa malata kwanu konko ndalama mumapeleka malata anu atafika,0993242921
$12