MALO ndi manyumba womwe

Pali Malo wogulisa pa Nkhotakota boma ndi manyumba womwe atatu.magetsi analowa kale madzi pafupi kufupiso ndi mseu watala.location sait Paus.nyumba yimodzi ya makomo awiri nyumba yiliyose zipinda ziwiri ndi stores.yayikulu yomwe yili payokha zipinda zitatu ndi stores.kuseli kwake kuli so Malo akulu woti kutha kukwanaso ma nyumba awiri.ndukufunapo 9,000 000 kwacha.kuvanaso kulipo.call or wap on 0994938024/0884129217

MK9,000,000

seller's name'
Name: Vehicle s
seller phone number
Location: Nkhotakota
uploaded on
Date: 22 February, 2024

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 5
product image 1
Image 2 of 5
product image 2
Image 3 of 5
product image 3
Image 4 of 5
product image 4
Image 5 of 5