Ngati mukufuna malo otsika mtengo ku lilongwe kuno ndiye Ali ku area 25 kwa kasengere Malowa size yake ndi 15 by 30 meters Mtengo wake ndi 1.3 million Ngati mukufuna kunkhala ndi Malo anu bwerani kuno kwa kasengere number imene mungandipeze ndi 0992335517 imeneyinso ili pa Whatsapp komanso ndili ndi ya TNM ya 0885837201 basi zantheka
FREE