Mulibwanji abale nda alongo kulikonse muli pano. Pa fb ine ndine agent wanu. Ndakhlandikukutumikira kunkhani ya ku sintha ndilama rands to kwacha Nkhani ndabwera pano siyapatali ndkupanga post mene ndimapangira muja ku program yosintha ndilama ija nawona. Post ina yake ya zimayi akukamba zokhuza moyo wake mene wadusa komano atakumana ndi gogo More
FREE