Malowa size yake ndi 15 by 30 meters ndipo ili ku mpanda Kuli quarters ndi nyumba yosamaliza ya three bedroom, sitting room, dinning room, kitchen, stores, bathroom ndi toilet Kuchoka mu tala kufika pa plot ndi two minutes Mabwana panja mumafuna malo ambali mwa mseu wa tala ndi amenewa mpanda ulipo mudzapitiliza chitukuko Ndalama ikufunika mwasangasanga choncho mtengo ndatsitsiratu tikufuna tikoze penapake Ngati mukufuna kudziwa zambiri ndiyimbireni pa 0992335517/0885837201
FREE