Self contained house ya zipinda zitatu, madzi ndi magetsi alipo kale komanso ili mbali mwa msewu. Ili mwa Mwambuli pafupi ndi mashop a Tob in Karonga. It's also negotiable
MWK9,500,000