Kodi mwakhala mukusaka malo oti mugule koma ali wotakasuka komaso a flat bwino? Yankho lanu lapezeka! Tili ndi malo ogulisa ku Nsaru okwana 5 Acres ndipo ali pafupi ndi msewu watala wa Kasiya osakwanaso 1km mwafika, nkhani ya madzi ndi magetsi sizilipatali. Only serious buyers Call or WhatsApp 0999206861 kuti timvane za mtengo komaso zina zambiri!
MWK9,000,000