Nissan Vanette F8 automatic transmission yogulisa. Inachita ngozi kutsogolo kuomba mtengo. Misonkho ilipo. Blue book ilipo. Ndiyamatayala awiri kumbuyo. Ndiyoyenda , mukawongolesa nokha. Ili kuno Tsangano Turns Ntcheu. Mtengo K1.8 million kukambirana pa ground. Whatsapp 0999050091.
$180