Toyota Porte 2008 model 2nz engine Misonkho yonse yabwino Ili mudzina langa No agent Imapanga utsi ndiye ndamasula head mukakonza nokha bvutolo, Engine and gearbox was intact oyamba kumasula ndineyo need fast cash 1.5million basi mtengo wanjinga yamoto 0994 189 322 Dzenza Area 25 Lilongwe Only serious buyers
MWK1,500